Qari
Murottal Audio
قُلْ هُوَ اللّٰهُ اَحَدٌۚ
qul huwallāhu aḥad(un).
Nenani (Muhammad), “Iye ndi Allah, Wamphamvu zonse.”
اَللّٰهُ الصَّمَدُۚ
allāhuṣ-ṣamad(u).
Mulungu ndiye malo opempha chilichonse.
لَمْ يَلِدْ وَلَمْ يُوْلَدْۙ
lam yalid wa lam yūlad.
(Mulungu) sanabereke ndipo sanabadwe.
وَلَمْ يَكُنْ لَّهٗ كُفُوًا اَحَدٌ ࣖ
wa lam yakul lahū kufuwan aḥad(un).
Ndipo palibe chofanana ndi Iye.”