17
Q.S Al-Layl (92:17)
وَسَيُجَنَّبُهَا الْاَتْقَىۙ
wa sayujannabuhal-atqā.
Ndipo wolungama kwambiri mwa iye adzatetezedwa ku gehena,
18
Q.S Al-Layl (92:18)
الَّذِيْ يُؤْتِيْ مَالَهٗ يَتَزَكّٰىۚ
allażī yu'tī mālahū yatazakkā.
amene akupereka chuma chake (m’njira ya Allah) kuti adziyeretse (yekha),
19
Q.S Al-Layl (92:19)
وَمَا لِاَحَدٍ عِنْدَهٗ مِنْ نِّعْمَةٍ تُجْزٰىٓۙ
wa mā li'aḥadin ‘indahū min ni‘matin tujzā.
ndipo palibe amene wamupatsa chisomo choti abwezere,
20
Q.S Al-Layl (92:20)
اِلَّا ابْتِغَاۤءَ وَجْهِ رَبِّهِ الْاَعْلٰىۚ
illabtigā'a wajhi rabbihil-a‘lā.
koma (anapereka yekha) chifukwa anafuna chisangalalo cha Mulungu wake Wam'mwambamwamba.
21
Q.S Al-Layl (92:21)
وَلَسَوْفَ يَرْضٰى ࣖ
wa lasaufa yarḍā.
Ndipo ndithudi mtsogolomu adzapeza chisangalalo (changwiro).