111
Q.S Ta-Ha (20:111)
۞ وَعَنَتِ الْوُجُوْهُ لِلْحَيِّ الْقَيُّوْمِۗ وَقَدْ خَابَ مَنْ حَمَلَ ظُلْمًا
wa ‘anatil-wujūhu lil-ḥayyil-qayyūm(i), wa qad khāba man ḥamala ẓulmā(n).
Ndipo nkhope zonse zinawerama pamaso pa (Allah) Wamoyo ndi Yekha. Ndi kutayika kwenikweni kwa anthu ochita zosalungama.
42
Q.S Ash-Shura (42:42)
اِنَّمَا السَّبِيْلُ عَلَى الَّذِيْنَ يَظْلِمُوْنَ النَّاسَ وَيَبْغُوْنَ فِى الْاَرْضِ بِغَيْرِ الْحَقِّۗ اُولٰۤىِٕكَ لَهُمْ عَذَابٌ اَلِيْمٌ
innamas-sabīlu ‘alal-lażīna yaẓlimūnan-nāsa wa yabgūna fil-arḍi bigairil-ḥaqq(i), ulā'ika lahum ‘ażābun alīm(un).
Ndithudi, kudzimva mlandu kuli kwa iwo okha amene amachitira anthu zinthu zopanda chilungamo ndi kupitirira malire padziko lapansi popanda (kusamala) choonadi. Iwo adalandira chilango chowawa.