19
Q.S Muhammad (47:19)
فَاعْلَمْ اَنَّهٗ لَآ اِلٰهَ اِلَّا اللّٰهُ وَاسْتَغْفِرْ لِذَنْۢبِكَ وَلِلْمُؤْمِنِيْنَ وَالْمُؤْمِنٰتِۚ وَاللّٰهُ يَعْلَمُ مُتَقَلَّبَكُمْ وَمَثْوٰىكُمْ ࣖ
fa‘lam annahū lā ilāha illallāhu wastagfir liżambika wa lil-u'minīna wal-u'mināt(i), wallāhu ya‘lamu mutaqallabakum wa maṡwākum.
Dziwani kuti palibe Mulungu (woyenera kupembedzedwa) koma Allah ndipo pemphani chikhululukiro cha machimo anu ndi machimo a okhulupirira, amuna ndi akazi. Ndipo Allah amadziwa malo anu ogwirira ntchito ndi malo okhala.