53
Q.S Al-Anfal (8:53)
ذٰلِكَ بِاَنَّ اللّٰهَ لَمْ يَكُ مُغَيِّرًا نِّعْمَةً اَنْعَمَهَا عَلٰى قَوْمٍ حَتّٰى يُغَيِّرُوْا مَا بِاَنْفُسِهِمْۙ وَاَنَّ اللّٰهَ سَمِيْعٌ عَلِيْمٌۙ
Żālika bi'annallāha lam yaku mugayyiran ni‘matan an‘amahā ‘alā qaumin ḥattā yugayyirū mā bi'anfusihim, wa annallāha samī‘un ‘alīm(un).
Izi zili choncho chifukwa chakuti Mulungu sadzasintha chisomo chimene wapereka kwa anthu, mpaka anthu atasintha zomwe zili mwa iwo okha. Ndithudi, Mulungu ndi Wakumva Zonse, Wodziwa Zonse,