52

Q.S Al-Anfal (8:52)

كَدَأْبِ اٰلِ فِرْعَوْنَۙ وَالَّذِيْنَ مِنْ قَبْلِهِمْۗ كَفَرُوْا بِاٰيٰتِ اللّٰهِ فَاَخَذَهُمُ اللّٰهُ بِذُنُوْبِهِمْۗ اِنَّ اللّٰهَ قَوِيٌّ شَدِيْدُ الْعِقَابِ

kada'bi āli fir‘aun(a), wal-lażīna min qablihim, kafarū bi'āyātillāhi fa akhażahumullāhu biżunūbihim, innallāha qawiyyun syadīdul-‘iqāb(i).

(Mkhalidwe wawo) unali wofanana ndi mkhalidwe wa otsatira a Farao ndi omwe adalipo kale. Iwo adakana ma Aya a Allah, kotero Allah adawalanga chifukwa cha machimo awo. Ndithudi, Allah ndi Wamphamvuzonse ndipo chilango Chake ndi choopsa kwambiri.