54

Q.S Al-Anfal (8:54)

كَدَأْبِ اٰلِ فِرْعَوْنَۙ وَالَّذِيْنَ مِنْ قَبْلِهِمْۚ كَذَّبُوْا بِاٰيٰتِ رَبِّهِمْ فَاَهْلَكْنٰهُمْ بِذُنُوْبِهِمْ وَاَغْرَقْنَآ اٰلَ فِرْعَوْنَۚ وَكُلٌّ كَانُوْا ظٰلِمِيْنَ

kada'bi āli fir‘aun(a), wal-lażīna min qablihim, każżabū bi'āyāti rabbihim fa ahlaknāhum biżunūbihim wa agraqnā āla fir‘aun(a), wa kullun kānū ẓālimīn(a).

(Mkhalidwe wawo) unali wofanana ndi wa otsatira a Farao ndi omwe adalipo kale. Iwo adakana mawu a Mbuye wawo, choncho tidawawononga chifukwa cha machimo awo ndipo tidamiza Farao ndi otsatira ake; chifukwa iwo ndi anthu osalungama.