130

Q.S Al-A'raf (7:130)

وَلَقَدْ اَخَذْنَآ اٰلَ فِرْعَوْنَ بِالسِّنِيْنَ وَنَقْصٍ مِّنَ الثَّمَرٰتِ لَعَلَّهُمْ يَذَّكَّرُوْنَ

wa laqad akhażnā āla fir‘auna bis-sinīna wa naqṣim minaṡ-ṡamarāti la‘allahum yażżakkarūn(a).

Ndipo ndithudi, Ife tamulanga Farao ndi anthu ake mwa kubweretsa zaka zambiri za chilala ndi kusowa kwa zipatso, kuti aphunzirepo kanthu.