129
Q.S Al-A'raf (7:129)
قَالُوْٓا اُوْذِيْنَا مِنْ قَبْلِ اَنْ تَأْتِيَنَا وَمِنْۢ بَعْدِ مَا جِئْتَنَا ۗقَالَ عَسٰى رَبُّكُمْ اَنْ يُّهْلِكَ عَدُوَّكُمْ وَيَسْتَخْلِفَكُمْ فِى الْاَرْضِ فَيَنْظُرَ كَيْفَ تَعْمَلُوْنَ ࣖ
qālū ūżīnā min qabli an ta'tiyanā wa mim ba‘di mā ji'tanā, qāla ‘asā rabbukum ay yuhlika ‘aduwwakum wa yastakhlifakum fil-arḍi fa yanẓura kaifa ta‘malūn(a).
Iwo (anthu a Mose) anati, “Tinazunzidwa (ndi Farao) musanatidzere ndi mutabwera.” (Mose) anayankha kuti, “Ndikukhulupirira kuti Ambuye wanu adzawononga adani anu ndikukupangani kukhala khalifa padziko lapansi; kenako adzaona momwe muchitire.”