131
Q.S Al-A'raf (7:131)
فَاِذَا جَاۤءَتْهُمُ الْحَسَنَةُ قَالُوْا لَنَا هٰذِهٖ ۚوَاِنْ تُصِبْهُمْ سَيِّئَةٌ يَّطَّيَّرُوْا بِمُوْسٰى وَمَنْ مَّعَهٗۗ اَلَآ اِنَّمَا طٰۤىِٕرُهُمْ عِنْدَ اللّٰهِ وَلٰكِنَّ اَكْثَرَهُمْ لَا يَعْلَمُوْنَ
fa iżā jā'athumul-ḥasanatu qālū lanā hāżihī, wa in tuṣibhum sayyi'atuy yaṭṭayyarū bimūsā wa mam ma‘ah(ū), alā innamā ṭā'iruhum ‘indallāhi wa lākinna aksṡarahum lā ya‘lamūn(a).
Ndipo ubwino ukawafika, amati, “Izi ndi chifukwa cha khama lathu.” Ndipo ngati anali m’mavuto, ankaimba mlandu Mose ndi omutsatira ake kuti ndi omwe achita tsoka. Dziwani kuti tsoka lawo lili m’manja mwa Allah, koma ambiri a iwo sadziwa.