45
Q.S Ali Imran (3:45)
اِذْ قَالَتِ الْمَلٰۤىِٕكَةُ يٰمَرْيَمُ اِنَّ اللّٰهَ يُبَشِّرُكِ بِكَلِمَةٍ مِّنْهُۖ اسْمُهُ الْمَسِيْحُ عِيْسَى ابْنُ مَرْيَمَ وَجِيْهًا فِى الدُّنْيَا وَالْاٰخِرَةِ وَمِنَ الْمُقَرَّبِيْنَۙ
iż qālatil-malā'ikatu yā maryama innallāha yubasysyiruki bikalimatim minhusmuhul-masīḥu ‘īsabnu maryama wajīhan fid-dun-yā wal-ākhirati wa minal-muqarrabīn(a).
(Kumbukirani) pamene angelo adati, “E iwe Mariya! Mulungu akukuuza nkhani yabwino ya mawu ochokera kwa Iye, dzina lake lidzakhala Mesiya, Yesu mwana wa Mariya, wolemekezeka padziko lapansi ndi pa Tsiku Lomaliza, ndi m’modzi mwa oyandikira (kwa Mulungu).