44

Q.S Ali Imran (3:44)

ذٰلِكَ مِنْ اَنْۢبَاۤءِ الْغَيْبِ نُوْحِيْهِ اِلَيْكَ ۗوَمَا كُنْتَ لَدَيْهِمْ اِذْ يُلْقُوْنَ اَقْلَامَهُمْ اَيُّهُمْ يَكْفُلُ مَرْيَمَۖ وَمَا كُنْتَ لَدَيْهِمْ اِذْ يَخْتَصِمُوْنَ

Żālika min ambā'il-gaibi nūḥīhi ilaik(a), wa mā kunta ladaihim iż yulqūna aqlāmahum ayyuhum yakfulu maryam(a), wa mā kunta ladaihim iż yakhtaṣimūn(a).

Imeneyo ndi nkhani zina zosaoneka zimene tinakuvumbulutsira iwe (Muhammad), ngakhale kuti sunali nawo pamene ankaponya mapeni awo (kuti achite maere) pa amene adzasunga Mariya mwa iwo, ndipo sunali nawo pamene ankakangana.