46

Q.S Ali Imran (3:46)

وَيُكَلِّمُ النَّاسَ فِى الْمَهْدِ وَكَهْلًا وَّمِنَ الصّٰلِحِيْنَ

wa yukallimun nāsa fil-mahdi wa kahlaw wa minaṣ-ṣāliḥīn(a).

ndipo ankalankhula ndi anthu (ali m'chibwana) ndi pamene anali wamkulu, ndipo anali m'gulu la anthu olungama.”