191

Q.S Ali Imran (3:191)

الَّذِيْنَ يَذْكُرُوْنَ اللّٰهَ قِيَامًا وَّقُعُوْدًا وَّعَلٰى جُنُوْبِهِمْ وَيَتَفَكَّرُوْنَ فِيْ خَلْقِ السَّمٰوٰتِ وَالْاَرْضِۚ رَبَّنَا مَا خَلَقْتَ هٰذَا بَاطِلًاۚ سُبْحٰنَكَ فَقِنَا عَذَابَ النَّارِ

al-lażīna yażkurūnallāha qiyāmaw wa qu‘ūdaw wa ‘alā junūbihim wa yatafakkarūna fi khalqis-samāwāti wal-arḍ(i), rabbanā mā khalaqta hāżā bāṭilā(n), subḥānaka fa qinā ‘ażāban-nār(i).

(ndiye) amene amakumbukira Allah ali chilili, atakhala kapena atagona, ndipo amaganizira za kulengedwa kwa thambo ndi dziko lapansi (akumati), "Mbuye wathu, simunalenge zonsezi pachabe, Ulemerero ukhale kwa Inu, titetezeni ku chilango cha kumoto."