192
Q.S Ali Imran (3:192)
رَبَّنَآ اِنَّكَ مَنْ تُدْخِلِ النَّارَ فَقَدْ اَخْزَيْتَهٗ ۗ وَمَا لِلظّٰلِمِيْنَ مِنْ اَنْصَارٍ
rabbanā innaka man tudkhilin-nāra faqad akhzaitah(ū), wa mā liẓ-ẓālimīna min anṣār(in).
Mbuye wathu, ndithudi, amene mwamuika ku Jahannama, ndiye kuti mwamunyoza, ndipo palibe wothandiza wochita zoipa.