190
Q.S Ali Imran (3:190)
اِنَّ فِيْ خَلْقِ السَّمٰوٰتِ وَالْاَرْضِ وَاخْتِلَافِ الَّيْلِ وَالنَّهَارِ لَاٰيٰتٍ لِّاُولِى الْاَلْبَابِۙ
inna fī khalqis-samāwāti wal-arḍi wakhtilāfil-laili wan-nahāri la'āyātil li'ulil-albāb(i).
Ndithudi, m'chilengedwe cha kumwamba ndi dziko lapansi, ndi kusinthana kwa usiku ndi usana pali zizindikiro (za ukulu wa Mulungu) kwa anthu ozindikira,