Revert to Islam, click here
Islam Al-Haq: Qur'an ndi Hadith
(Islam yeniyeni)



Topic - Jihad Harta rampasan perang dan fai' Pembagian harta rampasan perang Harta rampasan perang halal bagi tentara

Verse Search Results :
Total Verses : 3
69
Q.S Al-Anfal (8:69)

فَكُلُوْا مِمَّاغَنِمْتُمْ حَلٰلًا طَيِّبًاۖ وَّاتَّقُوا اللّٰهَ ۗاِنَّ اللّٰهَ غَفُوْرٌ رَّحِيْمٌ

fa kulū mimmā ganimtum ḥalālan ṭayyibā(n), wattaqullāh(a), innallāha gafūrur raḥīm(un).

Choncho idyani zina mwa zomwe mwapeza pankhondo, monga chakudya chovomerezeka ndi chabwino, ndipo opani Mulungu. Ndithudi, Mulungu ndi Wokhululuka, Wachifundo.


19
Q.S Al-Fath (48:19)

وَّمَغَانِمَ كَثِيْرَةً يَّأْخُذُوْنَهَا ۗ وَكَانَ اللّٰهُ عَزِيْزًا حَكِيْمًا

wa magānima kaṡīratay ya'khużūnahā, wa kānallāhu ‘azīzan ḥakīmā(n).

Ndipo adzalandira zofunkha zambiri za nkhondo. Ndipo Mulungu ndi Wamphamvu zonse, Wanzeru zonse.


20
Q.S Al-Fath (48:20)

وَعَدَكُمُ اللّٰهُ مَغَانِمَ كَثِيْرَةً تَأْخُذُوْنَهَا فَعَجَّلَ لَكُمْ هٰذِهٖ وَكَفَّ اَيْدِيَ النَّاسِ عَنْكُمْۚ وَلِتَكُوْنَ اٰيَةً لِّلْمُؤْمِنِيْنَ وَيَهْدِيَكُمْ صِرَاطًا مُّسْتَقِيْمًاۙ

wa‘adakumullāhu magānima kaṡīratan ta'khużūnahā fa‘ajjala lakum hāżihī wa kaffa aidiyan-nāsi ‘ankum, wa litakūna āyatal lil-mu'minīna wa yahdiyakum ṣirāṭam mustaqīmā(n).

Allah anakulonjezani zofunkha zambiri zankhondo zomwe mungathe kutenga, choncho anakufulumizitsirani izi (zofunkha zankhondo) ndipo analetsa manja a anthu (kuwonongani) (kuti muyamike Iye) ndi kuti zikhale umboni kwa okhulupirira ndi kuti akutsogolereni ku njira yowongoka.