وَاِذْ قَالَتِ الْمَلٰۤىِٕكَةُ يٰمَرْيَمُ اِنَّ اللّٰهَ اصْطَفٰىكِ وَطَهَّرَكِ وَاصْطَفٰىكِ عَلٰى نِسَاۤءِ الْعٰلَمِيْنَ
wa iż qālatil-malā'ikatu yā maryama innallāhaṣṭafāki wa ṭahharaki waṣṭafāki ‘alā nisā'il-‘ālamīn(a).
Ndipo (kumbukirani) pamene angelo adati, "Ewe Mariyamu! Ndithudi, Mulungu wakusankha, wakuyeretsa, ndipo wakuika patsogolo kuposa akazi onse padziko lonse lapansi (panthawiyo).
وَمَرْيَمَ ابْنَتَ عِمْرٰنَ الَّتِيْٓ اَحْصَنَتْ فَرْجَهَا فَنَفَخْنَا فِيْهِ مِنْ رُّوْحِنَا وَصَدَّقَتْ بِكَلِمٰتِ رَبِّهَا وَكُتُبِهٖ وَكَانَتْ مِنَ الْقٰنِتِيْنَ ࣖ ۔
wa maryamabnata ‘imrānal-latī aḥṣanat farjahā fa nafakhnā fīhi mir rūḥinā wa ṣaddaqat bikalimāti rabbihā wa kutubihī wa kānat minal-qānitīn(a).
ndi Mariyamu, mwana wamkazi wa Imran, amene adasunga ulemu wake, kenako tidauzira m'mimba mwake mzimu wathu (wolengedwa), ndipo adatsimikizira mawu a Mbuye wake ndi mabuku ake; ndipo anali m'modzi mwa anthu omvera.