فَلَمَّا وَضَعَتْهَا قَالَتْ رَبِّ اِنِّيْ وَضَعْتُهَآ اُنْثٰىۗ وَاللّٰهُ اَعْلَمُ بِمَا وَضَعَتْۗ وَلَيْسَ الذَّكَرُ كَالْاُنْثٰى ۚ وَاِنِّيْ سَمَّيْتُهَا مَرْيَمَ وَاِنِّيْٓ اُعِيْذُهَا بِكَ وَذُرِّيَّتَهَا مِنَ الشَّيْطٰنِ الرَّجِيْمِ
falammā waḍa‘athā qālat rabbi innī waḍa‘tuhā unṡā, wallāhu a‘lamu bimā waḍa‘at, wa laisaż-żakaru kal-unṡā, wa innī sammaituhā maryama wa innī u‘īżuhā bika wa żurriyyatahā minasy-syaiṭānir-rajīm(i).
Choncho pamene adamubereka, anati, “O Ambuye wanga, ndabereka mwana wamkazi.” Ngakhale kuti Allah amadziwa bwino zimene adabereka, ndipo amuna si ofanana ndi akazi. “Ndipo ndinamupatsa dzina lakuti Mariyamu, ndipo ndikupempha chitetezo Chanu kwa iye ndi ana ake ndi zidzukulu zake ku (kulowerera kwa) mdierekezi wotembereredwa.”