105
Q.S An-Nisa (4:105)
اِنَّآ اَنْزَلْنَآ اِلَيْكَ الْكِتٰبَ بِالْحَقِّ لِتَحْكُمَ بَيْنَ النَّاسِ بِمَآ اَرٰىكَ اللّٰهُ ۗوَلَا تَكُنْ لِّلْخَاۤىِٕنِيْنَ خَصِيْمًا ۙ
innā anzalnā ilaikal-kitāba bil-ḥaqqi litaḥkuma bainan-nāsi bimā arākallāh(u), wa lā takun lil-khā'inīna khaṣīmā(n).
Ndithudi, Takutumizirani Buku (Qur'an) lobweretsa choonadi, kuti muweruze pakati pa anthu motsatira zimene Mulungu wakuphunzitsani, ndipo musakhale mdani wa (munthu wosalakwa), chifukwa (kuteteza) munthu wopereka chinyengo,