2
Q.S Al-Mulk (67:2)
ۨالَّذِيْ خَلَقَ الْمَوْتَ وَالْحَيٰوةَ لِيَبْلُوَكُمْ اَيُّكُمْ اَحْسَنُ عَمَلًاۗ وَهُوَ الْعَزِيْزُ الْغَفُوْرُۙ
allażī khalaqal-mauta wal-ḥayāta liyabluwakum ayyukum aḥsanu ‘amalā(n), wa huwal-‘azīzul-gafūr(u).
Amene adalenga imfa ndi moyo, kuti akuyeseni kuti ndani mwa inu ali ndi zochita zabwino, ndipo Iye ndi Wamphamvu zonse, Wokhululuka kwambiri.