9
Q.S Al-Anfal (8:9)
اِذْ تَسْتَغِيْثُوْنَ رَبَّكُمْ فَاسْتَجَابَ لَكُمْ اَنِّيْ مُمِدُّكُمْ بِاَلْفٍ مِّنَ الْمَلٰۤىِٕكَةِ مُرْدِفِيْنَ
iż tastagīṡūna rabbakum fastajāba lakum annī mumiddukum bi'alfim minal-malā'ikati murdifīn(a).
(Kumbukirani), pamene mudapempha thandizo kwa Mbuye wanu, ndipo Iye adakulolani kuti, "Ndithudi, ndidzakubweretserani magulu olimbikitsa ndi angelo chikwi omwe adzabwera motsatizana."