7
Q.S An-Nur (24:7)
وَالْخَامِسَةُ اَنَّ لَعْنَتَ اللّٰهِ عَلَيْهِ اِنْ كَانَ مِنَ الْكٰذِبِيْنَ
wal-khāmisatu anna la‘natallāhi ‘alaihi in kāna minal-kāżibīn(a).
Ndipo lumbiro lachisanu ndi lakuti temberero la Allah lidzamugwera ngati ali m'gulu la abodza.
9
Q.S An-Nur (24:9)
وَالْخَامِسَةَ اَنَّ غَضَبَ اللّٰهِ عَلَيْهَآ اِنْ كَانَ مِنَ الصّٰدِقِيْنَ
wal-khāmisata anna gaḍaballāhi ‘alaihā in kāna minaṣ-ṣādiqīn(a).
ndi lumbiro lachisanu kuti mkwiyo wa Mulungu udzamugwera (mkaziyo), ngati mwamunayo (mwamuna wake) ali m'gulu la onena zoona.