10
Q.S Al-Buruj (85:10)
اِنَّ الَّذِيْنَ فَتَنُوا الْمُؤْمِنِيْنَ وَالْمُؤْمِنٰتِ ثُمَّ لَمْ يَتُوْبُوْا فَلَهُمْ عَذَابُ جَهَنَّمَ وَلَهُمْ عَذَابُ الْحَرِيْقِۗ
innal-lażīna fatanul-mu'minīna wal-mu'mināti ṡumma lam yatūbū fa lahum ‘ażābu jahannama wa lahum ‘ażābul-ḥarīq(i).
Ndithudi, amene amabweretsa mayesero (matsoka, kupha, kuzunza) kwa okhulupirira amuna ndi akazi koma osalapa, ndiye kuti adzalandira chilango cha ku Jahena ndipo adzalandira chilango (jahena) choyaka.