25
Q.S Al-Mutaffifin (83:25)
يُسْقَوْنَ مِنْ رَّحِيْقٍ مَّخْتُوْمٍۙ
yusqauna mir raḥīqim makhtūm(in).
Anapatsidwa kumwa vinyo woyera (wosaledzeretsa) womwe unali udakali wotsekedwa.
يُسْقَوْنَ مِنْ رَّحِيْقٍ مَّخْتُوْمٍۙ
yusqauna mir raḥīqim makhtūm(in).
Anapatsidwa kumwa vinyo woyera (wosaledzeretsa) womwe unali udakali wotsekedwa.