49

Q.S Al-Anfal (8:49)

اِذْ يَقُوْلُ الْمُنٰفِقُوْنَ وَالَّذِيْنَ فِيْ قُلُوْبِهِمْ مَّرَضٌ غَرَّ هٰٓؤُلَاۤءِ دِيْنُهُمْۗ وَمَنْ يَّتَوَكَّلْ عَلَى اللّٰهِ فَاِنَّ اللّٰهَ عَزِيْزٌ حَكِيْمٌ

iż yaqūlul-munāfiqūna wal-lażīna fī qulūbihim maraḍun garra hā'ulā'i dīnuhum, wa may yatawakkal ‘alallāhi fa innallāha ‘azīzun ḥakīm(un).

(Kumbukirani), pamene achinyengo ndi omwe ali ndi matenda m'mitima mwawo akunena kuti, "Iwo (okhulupirira) anyengedwa mu chipembedzo chawo." (Allah akunena), "Aliyense amene adalira Mulungu, dziwani kuti Mulungu ndi Wamphamvu Zonse, Wanzeru Zonse."