Q.S Al-Anfal (8:48)
وَاِذْ زَيَّنَ لَهُمُ الشَّيْطٰنُ اَعْمَالَهُمْ وَقَالَ لَا غَالِبَ لَكُمُ الْيَوْمَ مِنَ النَّاسِ وَاِنِّيْ جَارٌ لَّكُمْۚ فَلَمَّا تَرَاۤءَتِ الْفِئَتٰنِ نَكَصَ عَلٰى عَقِبَيْهِ وَقَالَ اِنِّيْ بَرِيْۤءٌ مِّنْكُمْ اِنِّيْٓ اَرٰى مَا لَا تَرَوْنَ اِنِّيْٓ اَخَافُ اللّٰهَ ۗوَاللّٰهُ شَدِيْدُ الْعِقَابِ ࣖ
wa iż zayyana lahumusy-syaiṭānu a‘mālahum wa qāla lā gāliba lakumul-yauma minan-nāsi wa innī jārul lakum, falammā tarā'atil-fi'atāni nakaṣa ‘alā ‘aqibaihi wa qāla innī barī'um minkum innī arā mā lā tarauna innī akhāfullāh(a), wallāhu syadīdul-‘iqāb(i).
Ndipo (kumbukirani) pamene Satana adawapangitsa kuti zochita zawo (zochimwa) ziwoneke zokongola ndipo adati, "Palibe amene angakugonjetseni lero, ndipo ndithudi, ine ndine mthandizi wanu." Choncho pamene magulu awiriwa adaonana (maso ndi maso), Satana adabwerera mmbuyo nati, "Ndithudi ndasiyana nanu; ndikuona zomwe simukuziona; ndithudi ine ndikuopa Mulungu." Mulungu ndi wolanga kwambiri.