25

Q.S Al-Anfal (8:25)

وَاتَّقُوْا فِتْنَةً لَّا تُصِيْبَنَّ الَّذِيْنَ ظَلَمُوْا مِنْكُمْ خَاۤصَّةً ۚوَاعْلَمُوْٓا اَنَّ اللّٰهَ شَدِيْدُ الْعِقَابِ

wattaqū fitnatal lā tuṣībannal-lażīna ẓalamū minkum khāṣṣah(tan), wa‘lamū annallāha syadīdul-‘iqāb(i).

Ndipo chenjerani ndi chilango chomwe sichidzagwera okhawo amene akuchita zoipa pakati panu. Dziwani kuti Mulungu ndi wolanga kwambiri.