24

Q.S Al-Anfal (8:24)

يٰٓاَيُّهَا الَّذِيْنَ اٰمَنُوا اسْتَجِيْبُوْا لِلّٰهِ وَلِلرَّسُوْلِ اِذَا دَعَاكُمْ لِمَا يُحْيِيْكُمْۚ وَاعْلَمُوْٓا اَنَّ اللّٰهَ يَحُوْلُ بَيْنَ الْمَرْءِ وَقَلْبِهٖ وَاَنَّهٗٓ اِلَيْهِ تُحْشَرُوْنَ

yā ayyuhal-lażīna āmanustajībū lillāhi wa lir-rasūli iżā da‘ākum limā yuḥyīkum, wa‘lamū annallāha yaḥūlu bainal-mar'i wa qalbihī wa annahū ilaihi tuḥsyarūn(a).

E inu amene mwakhulupirira! kwaniritsani pempho la Allah ndi Mtumiki, akakuitanani ku chinthu chomwe chimakupatsani moyo, ndipo dziwani kuti Allah wapanga malire pakati pa munthu ndi mtima wake ndipo ndithudi kwa Iye ndiko mudzasonkhanitsidwa.