21

Q.S Al-Insan (76:21)

عٰلِيَهُمْ ثِيَابُ سُنْدُسٍ خُضْرٌ وَّاِسْتَبْرَقٌۖ وَّحُلُّوْٓا اَسَاوِرَ مِنْ فِضَّةٍۚ وَسَقٰىهُمْ رَبُّهُمْ شَرَابًا طَهُوْرًا

‘Āliyahum ṡiyābu sundusin khuḍruw wa istabraq(un), wa ḥullū asāwira min fiḍḍah(tin), wa saqāhum rabbuhum syarāban ṭahūrā(n).

Anavala silika wobiriwira bwino ndi silika wokhuthala ndipo anavala zibangili zopangidwa ndi siliva, ndipo Mulungu anawapatsa chakumwa choyera (ndi chopatulika).