20

Q.S Al-Insan (76:20)

وَاِذَا رَاَيْتَ ثَمَّ رَاَيْتَ نَعِيْمًا وَّمُلْكًا كَبِيْرًا

wa iżā ra'aita ṡamma ra'aita na‘īmaw wa mulkan kabīrā(n).

Ndipo ngati muwona (mkhalidwe) kumeneko (kumwamba), ndithudi mudzawona mitundu yosiyanasiyana ya zosangalatsa ndi ufumu waukulu.