80
Q.S Al-A'raf (7:80)
وَلُوْطًا اِذْ قَالَ لِقَوْمِهٖٓ اَتَأْتُوْنَ الْفَاحِشَةَ مَا سَبَقَكُمْ بِهَا مِنْ اَحَدٍ مِّنَ الْعٰلَمِيْنَ
wa lūṭan iż qāla liqaumihī ata'tūnal-fāḥisyata mā sabaqakum bihā min aḥadim minal-‘ālamīn(a).
Ndipo (tidatumizanso) Luti, pamene adauza anthu ake kuti, “Bwanji mukuchita chinthu chonyansa chomwe palibe amene adachitapo kale (padziko lapansi)?”