79
Q.S Al-A'raf (7:79)
فَتَوَلّٰى عَنْهُمْ وَقَالَ يٰقَوْمِ لَقَدْ اَبْلَغْتُكُمْ رِسَالَةَ رَبِّيْ وَنَصَحْتُ لَكُمْ وَلٰكِنْ لَّا تُحِبُّوْنَ النّٰصِحِيْنَ
fa tawallā ‘anhum wa qāla yā qaumi laqad ablagtukum risālata rabbī wa naṣaḥtu lakum wa lākil lā tuḥibbūnan-nāṣiḥīn(a).
Kenako (Saleh) anawasiya, nati, "E inu anthu anga! Ndithudi, ndakufikitsirani uthenga wa Mbuye wanga ndipo ndakulangizani. Koma simukonda anthu opereka uphungu."