49
Q.S Al-A'raf (7:49)
اَهٰٓؤُلَاۤءِ الَّذِيْنَ اَقْسَمْتُمْ لَا يَنَالُهُمُ اللّٰهُ بِرَحْمَةٍۗ اُدْخُلُوا الْجَنَّةَ لَا خَوْفٌ عَلَيْكُمْ وَلَآ اَنْتُمْ تَحْزَنُوْنَ
ahā'ulā'il-lażīna aqsamtum lā yanāluhumullāhu biraḥmah(tin), udkhulul-jannata lā khaufun ‘alaikum wa lā antum taḥzanūn(a).
Kodi awa ndi anthu amene munalumbira kuti sadzalandira chifundo kuchokera kwa Mulungu?” (Allah anati), “Lowani ku Paradaiso! Sipadzakhala mantha kwa inu, ndipo simudzadandaula.”