48
Q.S Al-A'raf (7:48)
وَنَادٰٓى اَصْحٰبُ الْاَعْرَافِ رِجَالًا يَّعْرِفُوْنَهُمْ بِسِيْمٰىهُمْ قَالُوْا مَآ اَغْنٰى عَنْكُمْ جَمْعُكُمْ وَمَا كُنْتُمْ تَسْتَكْبِرُوْنَ
wa nādā aṣḥābul-a‘rāfi rijālay ya‘rifūnahum bisīmāhum qālū mā agnā ‘ankum jam‘ukum wa mā kuntum tastakbirūn(a).
Ndipo anthu amene anali pamwamba pa A'raf (malo okwezeka kwambiri) ankaitana anthu amene ankawadziwa ndi zizindikiro, ponena kuti, "Chuma chimene mwasonkhanitsa ndi chimene mukudzitama nacho, (zikupezeka kuti) sichikuthandizani."