168

Q.S Al-A'raf (7:168)

وَقَطَّعْنٰهُمْ فِى الْاَرْضِ اُمَمًاۚ مِنْهُمُ الصّٰلِحُوْنَ وَمِنْهُمْ دُوْنَ ذٰلِكَ ۖوَبَلَوْنٰهُمْ بِالْحَسَنٰتِ وَالسَّيِّاٰتِ لَعَلَّهُمْ يَرْجِعُوْنَ

wa qaṭṭa‘nāhum fil-arḍi umamā(n), minhumuṣ-ṣāliḥūna wa minhum dūna żālik(a), wa balaunāhum bil-ḥasanāti was-sayyi'āti la‘allahum yarji‘ūn(a).

Ndipo tidawagawa m'magulu angapo padziko lapansi; pakati pawo pali anthu oopa Mulungu ndipo palinso omwe sali oopa Mulungu. Ndipo tidawayesa ndi zabwino ndi zoipa (matsoka), kuti abwerere (ku choonadi).