167
Q.S Al-A'raf (7:167)
وَاِذْ تَاَذَّنَ رَبُّكَ لَيَبْعَثَنَّ عَلَيْهِمْ اِلٰى يَوْمِ الْقِيٰمَةِ مَنْ يَّسُوْمُهُمْ سُوْۤءَ الْعَذَابِۗ اِنَّ رَبَّكَ لَسَرِيْعُ الْعِقَابِۖ وَاِنَّهٗ لَغَفُوْرٌ رَّحِيْمٌ
wa iż ta'ażżana rabbuka layab‘aṡanna ‘alaihim ilā yaumil-qiyāmati may yasūmuhum sū'al-‘ażāb(i), inna rabbaka lasarī‘ul-‘iqāb(i), wa innahū lagafūrur raḥīm(un).
Ndipo (kumbukira), pamene Mbuye wako adalengeza kuti adzatumiza anthu omwe adzawalanga kwambiri (Ayuda) mpaka Tsiku la Chiweruzo. Ndithudi, Mbuye wako ndi wofulumira kulanga, ndipo ndithudi Iye ndi Wokhululuka Kwambiri, Wachifundo Chambiri.