152
Q.S Al-A'raf (7:152)
اِنَّ الَّذِيْنَ اتَّخَذُوا الْعِجْلَ سَيَنَالُهُمْ غَضَبٌ مِّنْ رَّبِّهِمْ وَذِلَّةٌ فِى الْحَيٰوةِ الدُّنْيَاۗ وَكَذٰلِكَ نَجْزِى الْمُفْتَرِيْنَ
innal-lażīnattakhażul-‘ijla sayanāluhum gaḍabum mir rabbihim wa żillatun fil-ḥayātid-dun-yā, wa każālika najzil-muftarīn(a).
Ndithudi, iwo amene apanga (chifaniziro cha) mwana wa ng'ombe (monga kulambira kwawo), tsiku lina adzalandira mkwiyo wochokera kwa Mbuye wawo ndi kunyozedwa m'moyo uno padziko lapansi. Motero Timawalipira iwo amene amanena bodza.