151
Q.S Al-A'raf (7:151)
قَالَ رَبِّ اغْفِرْ لِيْ وَلِاَخِيْ وَاَدْخِلْنَا فِيْ رَحْمَتِكَ ۖوَاَنْتَ اَرْحَمُ الرّٰحِمِيْنَ ࣖ
qāla rabbigfirlī wa li'akhī wa adkhilnā fī raḥmatik(a), wa anta arḥamur-rāḥimīn(a).
Iye (Mose) anapemphera kuti, "Mbuye wanga, ndikhululukireni ine ndi m'bale wanga ndipo mutilowetse m'chifundo chanu, ndipo Inu ndinu Wachifundo kwambiri kuposa onse achifundo."