141
Q.S Al-A'raf (7:141)
وَاِذْ اَنْجَيْنٰكُمْ مِّنْ اٰلِ فِرْعَوْنَ يَسُوْمُوْنَكُمْ سُوْۤءَ الْعَذَابِۚ يُقَتِّلُوْنَ اَبْنَاۤءَكُمْ وَيَسْتَحْيُوْنَ نِسَاۤءَكُمْۗ وَفِيْ ذٰلِكُمْ بَلَاۤءٌ مِّنْ رَّبِّكُمْ عَظِيْمٌ ࣖ
wa iż anjainākum min āli fir‘auna yasūmūnakum sū'al-‘ażāb(i), yuqattilūna abnā'akum wa yastaḥyūna nisā'akum wa fī żālikum balā'um mir rabbikum ‘aẓīm(un).
Ndipo (kumbukirani, Inu Ana a Israeli) pamene tidakupulumutsani kwa (Farao) ndi anthu ake, omwe adakuzunzani kwambiri, adapha ana anu aamuna ndikusiya miyoyo ya ana anu aakazi. Ndipo pamenepo ndi mayeso aakulu ochokera kwa Mbuye wanu.