140
Q.S Al-A'raf (7:140)
قَالَ اَغَيْرَ اللّٰهِ اَبْغِيْكُمْ اِلٰهًا وَّهُوَ فَضَّلَكُمْ عَلَى الْعٰلَمِيْنَ
qāla agairallāhi abgīkum ilāhaw wa huwa faḍḍalakum ‘alal-‘ālamīn(a).
Iye (Mose) anati, "Kodi ndikoyenera kuti ndikufunireni mulungu wina kupatula Allah, ngakhale kuti Iye ndiye amene anakuikani patsogolo kuposa anthu onse (panthawiyo)?"