7
Q.S At-Taghabun (64:7)
زَعَمَ الَّذِيْنَ كَفَرُوْٓا اَنْ لَّنْ يُّبْعَثُوْاۗ قُلْ بَلٰى وَرَبِّيْ لَتُبْعَثُنَّ ثُمَّ لَتُنَبَّؤُنَّ بِمَا عَمِلْتُمْۗ وَذٰلِكَ عَلَى اللّٰهِ يَسِيْرٌ
za‘amal-lażīna kafarū allay yub‘aṡū, qul balā wa rabbī latub‘aṡunna ṡumma latunabba'unna bimā ‘amiltum, wa żālika ‘alallāhi yasīr(un).
Amene sakhulupirira akuganiza kuti sadzaukitsidwa. Nena (iwe Muhammad), "Iyayi, ndikulumbira kwa Mbuye wanga, ndithudi mudzaukitsidwa, kenako mudzauzidwa zonse zomwe mudachita." Ndipo zimenezo kwa Allah n'zosavuta.