6

Q.S At-Taghabun (64:6)

ذٰلِكَ بِاَنَّهٗ كَانَتْ تَّأْتِيْهِمْ رُسُلُهُمْ بِالْبَيِّنٰتِ فَقَالُوْٓا اَبَشَرٌ يَّهْدُوْنَنَاۖ فَكَفَرُوْا وَتَوَلَّوْا وَّاسْتَغْنَى اللّٰهُ ۗوَاللّٰهُ غَنِيٌّ حَمِيْدٌ

Żālika bi'annahū kānat ta'tīhim rusuluhum bil-bayyināti fa qālū abasyaruy yahdūnanā, fa kafarū wa tawallau wastagnallāh(u), wallāhu ganiyyun ḥamīd(un).

Izi zili choncho chifukwa chakuti atumwi atawadzera (kubweretsa) uthenga, anati, “Kodi n’koyenera kuti anthu atitsogolere?” Kenako anakana ndipo anabwerera m’mbuyo, ngakhale kuti Mulungu sakuwafuna. Ndipo Mulungu ndi Wolemera Kwambiri, Woyamikidwa Kwambiri.”