22

Q.S An-Nisa (4:22)

وَلَا تَنْكِحُوْا مَا نَكَحَ اٰبَاۤؤُكُمْ مِّنَ النِّسَاۤءِ اِلَّا مَا قَدْ سَلَفَ ۗ اِنَّهٗ كَانَ فَاحِشَةً وَّمَقْتًاۗ وَسَاۤءَ سَبِيْلًا ࣖ

wa lā tankiḥū mā nakaḥa ābā'ukum minan-nisā'i illā mā qad salaf(a), innahū kāna fāḥisyataw wa maqtā(n), wa sā'a sabīlā(n).

Ndipo musakwatire mkazi amene abambo anu adamukwatira, kupatula kale lomwe. Ndithudi, kuchita kumeneku n’koipa kwambiri ndipo n’kodedwa (ndi Allah) ndipo ndi njira yoipa kwambiri.