21

Q.S An-Nisa (4:21)

وَكَيْفَ تَأْخُذُوْنَهٗ وَقَدْ اَفْضٰى بَعْضُكُمْ اِلٰى بَعْضٍ وَّاَخَذْنَ مِنْكُمْ مِّيْثَاقًا غَلِيْظًا

wa kaifa ta'khużūnahū wa qad afḍā ba‘ḍukum ilā ba‘ḍiw wa akhażna minkum mīṡāqan galīẓā(n).

Ndipo mubweza bwanji pamene mwakhala mukugonana (monga mwamuna ndi mkazi), ndipo iwo (akazi anu) atenga pangano lamphamvu (ukwati) kwa inu?