135

Q.S An-Nisa (4:135)

۞ يٰٓاَيُّهَا الَّذِيْنَ اٰمَنُوْا كُوْنُوْا قَوَّامِيْنَ بِالْقِسْطِ شُهَدَاۤءَ لِلّٰهِ وَلَوْ عَلٰٓى اَنْفُسِكُمْ اَوِ الْوَالِدَيْنِ وَالْاَقْرَبِيْنَ ۚ اِنْ يَّكُنْ غَنِيًّا اَوْ فَقِيْرًا فَاللّٰهُ اَوْلٰى بِهِمَاۗ فَلَا تَتَّبِعُوا الْهَوٰٓى اَنْ تَعْدِلُوْا ۚ وَاِنْ تَلْوٗٓا اَوْ تُعْرِضُوْا فَاِنَّ اللّٰهَ كَانَ بِمَا تَعْمَلُوْنَ خَبِيْرًا

yā ayyuhal-lażīna āmanū kūnū qawwāmīna bil-qisṭi syuhadā'a lillāhi wa lau ‘alā anfusikum awil-wālidaini wal-aqrabīn(a), iy yakun ganiyyan au faqīran fallāhu aulā bihimā, falā tattabi‘ul-hawā an ta‘dilū, wa in talwū au tu‘riḍū fa innallāha kāna bimā ta‘malūna khabīrā(n).

Inu amene mwakhulupirira! Khalani ochirikiza chilungamo, mboni za Allah, ngakhale chitakhala chotsutsana ndi inu nokha kapena makolo anu ndi achibale anu. Kaya wotsutsidwayo ndi wolemera kapena wosauka, Allah amadziwa bwino zomwe zili zabwino kwa iye. Choncho musatsatire zofuna zanu, kufuna kupotoza choonadi. Ndipo ngati mupotoza (umboni) kapena kukana kuupereka, dziwani kuti Allah ndi wodziwa zonse zomwe mukuchita.