134
Q.S An-Nisa (4:134)
مَنْ كَانَ يُرِيْدُ ثَوَابَ الدُّنْيَا فَعِنْدَ اللّٰهِ ثَوَابُ الدُّنْيَا وَالْاٰخِرَةِ ۗوَكَانَ اللّٰهُ سَمِيْعًاۢ بَصِيْرًا ࣖ
man kāna yurīdu ṡawābad-dun-yā fa ‘indallāhi ṡawābud-dun-yā wal-ākhirah(ti), wa kānallāhu samī‘am baṣīrā(n).
Aliyense amene akufuna mphoto ya dziko lapansi, adziwe kuti kwa Mulungu kuli mphoto ya dziko lapansi ndi ya tsiku lomaliza. Ndipo Mulungu ndi Wakumva Zonse, Wakuona Zonse.