130
Q.S An-Nisa (4:130)
وَاِنْ يَّتَفَرَّقَا يُغْنِ اللّٰهُ كُلًّا مِّنْ سَعَتِهٖۗ وَكَانَ اللّٰهُ وَاسِعًا حَكِيْمًا
wa iy yatafarraqā yugnillāhu kullam min sa‘atih(ī), wa kānallāhu wāsi‘an ḥakīmā(n).
Ndipo ngati awiriwa alekana, Mulungu adzawapatsa aliyense wa iwo chikwaniro kuchokera ku chisomo Chake. Ndipo Mulungu ndi Wamphamvu Zonse, Wanzeru Kwambiri.