129
Q.S An-Nisa (4:129)
وَلَنْ تَسْتَطِيْعُوْٓا اَنْ تَعْدِلُوْا بَيْنَ النِّسَاۤءِ وَلَوْ حَرَصْتُمْ فَلَا تَمِيْلُوْا كُلَّ الْمَيْلِ فَتَذَرُوْهَا كَالْمُعَلَّقَةِ ۗوَاِنْ تُصْلِحُوْا وَتَتَّقُوْا فَاِنَّ اللّٰهَ كَانَ غَفُوْرًا رَّحِيْمًا
wa lan tastaṭī‘ū an ta‘dilū bainan-nisā'i wa lau ḥaraṣtum falā tamīlū kullal-maili fa tażarūhā kal-mu‘allaqah(ti), wa in tuṣliḥū wa tattaqū fa innallāha kāna gafūrar raḥīmā(n).
Ndipo simudzatha kuchita chilungamo pakati pa akazi anu, ngakhale mutafunitsitsa kutero, choncho musakokere kwambiri (kwa amene mumamukonda) mpaka kumusiya winayo atapachikidwa. Ndipo ngati musintha ndi kudziteteza (ku zoipa), ndithudi Mulungu ndi Wokhululuka Kwambiri, Wachifundo Chambiri.