22
Q.S As-Sajdah (32:22)
وَمَنْ اَظْلَمُ مِمَّنْ ذُكِّرَ بِاٰيٰتِ رَبِّهٖ ثُمَّ اَعْرَضَ عَنْهَا ۗاِنَّا مِنَ الْمُجْرِمِيْنَ مُنْتَقِمُوْنَ ࣖ
wa man aẓlamu mimman żukkira bi'āyāti rabbihī ṡumma a‘raḍa ‘anhā, innā minal-mujrimīna muntaqimūn(a).
Ndipo ndani woipa kwambiri kuposa amene wachenjezedwa ndi mawu a Mbuye wake, kenako nkuwasiya? Ndithudi, tidzawalipira anthu ochimwa.